Mawu a M'munsi
a Akatswiri a zaumoyo amachenjeza kuti kugwira ndi kudya nyama zam’tchire kungathenso kufalitsa matenda oopsa kwambiri monga anthrax ndi Ebola, ndi tizilombo tina tofanana ndi kachilombo ka HIV, kuchoka ku nyama kupita kwa anthu.