Mawu a M'munsi
a Ambiri mwa masamba amenewa ndiponso mabungwe ambiri amanena kuti salimbikitsa atsikana kuti asamadye kwambiri kuti azikhala oonda. Koma ena amasonyeza kuti moyo umenewu si vuto ndipo munthu amachita kusankha yekha. Mafomu opezeka pamasamba amenewa amafotokoza mmene munthu angabisire kwa makolo ake kulemera kwake kwenikweni komanso vuto lake la kadyedwe.