Mawu a M'munsi
b Onani magazini yapadera ya Galamukani! ya November 2007, imene inafotokoza nkhani yakuti “Kodi Tiyenera Kukhulupirira Baibulo?” Nkhani za m’magazini imeneyi zinafotokoza umboni wa ofukula zinthu zakale, akatswiri a mbiri yakale, asayansi ndiponso umboni wina wosonyeza kuti Baibulo ndi louziridwadi ndi Mulungu.