Mawu a M'munsi
b Nkhani ino ikungofotokoza mwachidule njira zosiyanasiyana zounikira matenda m’malo mopanga opaleshoni ndipo ikufotokozanso ubwino wa njirazi ndiponso mavuto ake. Kuti mudziwe zambiri pankhani imeneyi, werengani mabuku amene amafotokoza zimenezi kapena kafunseni kuchipatala.