Mawu a M'munsi
c Ngati mukuona kuti Yehova sangamve mapemphero anu chifukwa munachita tchimo lalikulu, muyenera kuuza makolo anu. Ndiponso ‘itanani akulu a mpingo [kuti akuthandizeni].’ (Yakobe 5:14) Akulu angakuthandizeni kuti mukhalenso ndi ubwenzi wabwino ndi Yehova.