Mawu a M'munsi
a Mpweya wabwino umene nyama ndi anthufe timagwiritsa ntchito umapezekanso m’madzi, m’zakudya zina komanso mu mpweya woipa umene timatulutsa. Choncho mpweya umene timapuma umayenda mogwirizana ndi kayendedwe ka madzi ndi mpweya umene zomera zimapuma.