Mawu a M'munsi
a Tikudziwa kuti aliyense amalakwitsa. (Aroma 3:23) Choncho ngati mnzanu wakulakwirani koma wakupepesani kuchokera pansi pamtima, muzikumbukira kuti “chikondi chimakwirira machimo ochuluka.”—1 Petulo 4:8.