Mawu a M'munsi
b Ngati mumamwa mankhwala akuchipatala chifukwa cha vuto la kuvutika maganizo, matenda a maganizo ochititsa munthu kusinthasintha zochita, kapena matenda ena okhudza ubongo, ndiye kuti vuto lanu ndi losiyana ndi la Valerie. Choncho, musasinthe mankhwala popanda kukambirana ndi dokotala.