Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti matendawa amatha kuchititsa munthu kuti apite padera, amayi ambiri amene amadwala matendawa amatha kubereka ana athanzi. Komabe, ndi bwino kuti amayi a pakati omwe ali ndi matendawa azilandira mankhwala omwe angawathandize kubereka ana athanzi.