Mawu a M'munsi
b T3 imaimira triiodothyronine ndipo T4 imaimira thyroxine. Nambala ya 3 ndiponso 4 ikuimira nambala ya ma atomu a ayodini amene amapezeka mu timadzito. Chithokomiro chimatulutsanso timadzi totchedwa calcitonin, tomwe timathandiza magazi kukhala ndi kasiyamu wokwanira.