Mawu a M'munsi
a Mankhwala amenewa amawapopera m’chiberekero ndipo mwana wosabadwayo akawamwa amafa, nthawi zambiri pasanapite maola awiri. Ndiyeno pakapita maola 24, mayiyo amabereka mwana wakufa, kapena mwana amene watsala pang’ono kufa.