Mawu a M'munsi
a Ngati mukufuna kuphunzira Baibulo kwaulere, panthawi ndi malo amene mungakonde, pitani ku Nyumba ya Ufumu ya Mboni za Yehova kapena lemberani kalata ofesi ya nthambi pa adiresi yomwe ili patsamba 5. Kapena fufuzani Mboni za Yehova pa Intaneti pogwiritsa ntchito adiresi iyi: www.jw.org.