Mawu a M'munsi
a Ngati mukufuna kudziwa ngati Mkhristu ayenera kupewa kumwa khofi kapena tiyi chifukwa chakuti amakhala ndi mankhwala a caffeine, amene amachititsa kuti munthu azingofuna kumwa khofi kapena tiyi, werengani nkhani yakuti “Mafunso Ochokera kwa Owerenga” mu Nsanja ya Olonda ya April 15, 2007.