Mawu a M'munsi
a Princip anapha mkazi wa Ferdinand mwangozi. Iye ankafuna kupha mkulu wa asilikali, yemwenso anali gavanala wa dera la Bosnia, dzina lake Oskar Potiorek, koma anamuphonya. Mkuluyu anali m’galimoto limodzi ndi banja lachifumuli.