Mawu a M'munsi
a M’nthawi ya atumwi oyang’anira amene ankayendera mipingo nthawi zina ‘ankapeza zochirikiza moyo mwa uthenga wabwino.’ Iwo ankalandiridwa m’nyumba za anthu ndi kulandira zopereka zimene anthu ankawapatsa mwa kufuna kwawo.—1 Akorinto 9:14.