Mawu a M'munsi
b Chitsanzo cha zinthu ngati zimenezi ndi kupereka ndalama kwa ansembe kuti munthu akhululukidwe machimo ake, nkhanza za khoti la tchalitchi cha Katolika, ndiponso kuwotchedwa kwa Mabaibulo ndi azibusa amene sankafuna kuti anthu awo aziwerenga okha Mawu a Mulungu.—Onani Nsanja ya Olonda ya November 15, 2002, tsamba 27.