Mawu a M'munsi
a Achinyamata amene amakonda kukhala okhaokha akuchuluka kwambiri ku Japan moti apatsidwa dzina lakuti hikikomori (munthu amene amangodzitsekera m’nyumba). Anthu ena akuganizira kuti anthu oterewa alipo pakati pa 500,000 ndi 1,000,000 ku Japan.