Mawu a M'munsi
a Buku lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova lili ndi mfundo zabwino za m’Baibulo zimene zingathandize achinyamata kuti athane ndi mavuto amene amakumana nawo. Mfundo zina zimapezeka pa Intaneti, pa adiresi iyi: www.pr418.com.