Mawu a M'munsi
c Malinga ndi zimene Baibulo limanena, banja lingathe ngati mmodzi wachita chigololo. Ndipo zikatere, winayo atha kukwatiranso. (Mateyo 19:9) Wina akachita chigololo, mwamuna kapena mkazi wake ndi amene ali ndi ufulu wosankha kuthetsa banjalo, koma osati achibale kapena anthu ena.—Agalatiya 6:5.