Mawu a M'munsi
b Achinyamata ena amatumiza kwa anzawo pa foni zithunzi zolaula zosonyeza iwowo. Khalidwe limeneli ndi loipa ndipo limasonyeza kupanda nzeru, chifukwa kaya cholinga chawo potumizapo ndi chotani, anthu ena akhoza kuziona.