Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b Nkhalango imeneyi inayamba kutetezedwa mu 1979 ndipo poyamba inkadziwika ndi dzina lakuti Huanchaca. Nkhalangoyi anaipatsa dzina latsopano mu 1988 pokumbukira wasayansi wina wa ku Bolivia dzina lake Noel Kempff Mercado. Wasayansiyu anaphedwa m’nkhalangoyi ndi anthu ozembetsa mankhwala osokoneza bongo, iye atatulukira mwangozi malo amene anthuwa ankakonzera mankhwalawa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena