Mawu a M'munsi
a Zinthu zoipa zimene zimachitika komanso mavuto amene anthufe timakumana nawo, zimachititsa anthu ambiri kukayikira zoti pali Mlengi amene amatikonda. Pankhani imeneyi, onani mutu 11 m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.