Mawu a M'munsi
a Pofuna kuthandiza mabanja, Mboni za Yehova zinatulutsa buku la masamba 192 lakuti Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja. Mukafuna kudziwa zambiri, lemberani Mboni za Yehova pa adiresi yoyenerera pa maadiresi amene ali patsamba 5 la magazini ino.