Mawu a M'munsi
c Anthu a mtundu wa Kayan anabwera ku Thailand kuchokera ku Myanmar. Panopa ku Myanmar kuli anthu a mtundu umenewu okwana 50,000 ndipo amadziwika ndi dzina lakuti Padaung, kutanthauza “Makosi Aatali.”