Mawu a M'munsi
a Komanso, udindo wa mwamuna mumpingo uli ndi malire. Iye ayenera kugonjera Khristu ndiponso kuchita zinthu motsatira mfundo za m’Baibulo. (1 Akorinto 11:3) Anthu amene ali ndi udindo mumpingo ayeneranso ‘kugonjerana wina ndi mnzake,’ ndipo ayenera kukhala odzichepetsa komanso ochita zinthu mogwirizana.—Aefeso 5:21.