Mawu a M'munsi
a Ngati mulibe Baibulo koma mumagwiritsa ntchito Intaneti, mukhoza kuwerenga Baibulo pa adiresi iyi: www.pr418.com. Pa adiresi imeneyi mukapezapo bokosi la mutu wakuti, “Werengani Baibulo pa Intaneti.” Palinso mabuku ofotokoza Baibulo m’zinenero zoposa 380.