Mawu a M'munsi
a Mboni za Yehova sizinangopeka dzina lakuti “Yehova” limeneli. Kuyambira kale kwambiri, dzina la Mulungu lakuti “Yehova” lakhala likulembedwa m’zinenero zina zimene sizinagwiritsidwe ntchito polemba Baibulo koyambirira, monga Chingelezi ndi Chijeremani. Koma n’zomvetsa chisoni kuti anthu ena omasulira Baibulo masiku ano achotsa dzina la Mulungu m’Mabaibulo awo ndipo m’malomwake aikamo mawu monga “Mulungu” kapena “Ambuye.” Zimenezi zikusonyeza kuti anthu amenewa salemekeza Mlembi Wamkulu wa Baibulo.