Mawu a M'munsi
a C.E. ndi mawu achidule achingelezi oimira “Common Era” omwe amatanthauza “M’nyengo Yathu Ino.” Ngati mukufuna kudziwa zambiri za ulosi wa Danieli wokhudza Mesiya, onani buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? patsamba 198.