Mawu a M'munsi
b Popeza matenda a kolera amayamba chifukwa cha kudya zakudya zoipa kapena kumwa madzi oipa, kuti munthu apewe matendawa ayenera kusamala ndi zimene amadya kapena kumwa. Kumwa madzi othira mankhwala komanso kudya zakudya zophikidwa mokwanira kumathandiza kupewa matendawa.