a Mukafuna kudziwa mfundo zomveka bwino za m’Baibulo zofotokoza chifukwa chake Mulungu walola kuti zoipa zizichitika, werengani mutu 11 wa buku lophunzirira Baibulo lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.