Mawu a M'munsi
a Zikuoneka kuti Yesu anabadwa m’mwezi wa Etanimu, malinga ndi kalendala yachiyuda (September-October, malinga ndi kalendala ya masiku ano). Onani buku lakuti Insight on the Scriptures, Voliyumu 2, tsamba 56, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.