Mawu a M'munsi
c Ngati mukufuna kudziwa zambiri pa nkhani imeneyi, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingapewe Bwanji Mtima Wofuna Kugonana ndi Amuna Kapena Akazi Anzanga?” m’mutu 28 wa buku lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.