Mawu a M'munsi
a Pambuyo pa ulamuliro wa Mfumu Solomo, ufumu wa Isiraeli, womwe unali ndi mafuko 12, unagawanika. Fuko la Yuda ndi la Benjamini linapanga ufumu wakum’mwera, ndipo mafuko ena 10 anapanga ufumu wakumpoto. Mzinda wa Yerusalemu unali likulu la ufumu wakum’mwera, ndipo mzinda wa Samariya unali likulu la ufumu wakumpoto.