Mawu a M'munsi
a Bukuli limadziwika ndi mayina otsatirawa: Book of Martyrs, That Is, a Collection of Several Martyrs Who Endured Death in the Name of Our Lord Jesus Christ, From Jan Hus Until This Year, 1554; Le Livre des martyrs; ndi Histoire des martyrs. Anthu ena analikonza bukuli mwina ndi mwina n’kulifalitsanso, pamene ena anawonjezeramo nkhani zina komanso zinthu zina ndi zina. Zimenezi zinachitika Crespin ali moyo komanso atamwalira.