Mawu a M'munsi
b Mabuku ena awiri okhala ndi mayina a anthu amene anafera chikhulupiriro chawo anafalitsidwanso m’chaka cha 1554. Buku la Crespin lakuti Book of Martyrs linafalitsidwanso m’chaka chimenechi. Limodzi mwa mabukuwa linalembedwa m’Chijeremani ndi Ludwig Rabus ndipo lina linalembedwa m’Chilatini ndi John Foxe.