Mawu a M'munsi
a Munthu amene mumam’konda akamwalira, ndi bwino kupewa kuchita zinthu mopupuluma, monga kusamukira nyumba ina kapena kuganiza zokwatiranso. Muyenera kuchita zinthu zimenezi patapita nthawi yokwanira.