Mawu a M'munsi
a Ngati muli ndi chidwi chofuna kudziwa ngati zinthu zinachita kulengedwa kapena kusanduka, mungawerenge kabuku ka m’chingelezi kakuti Was Life Created? ndiponso kakuti The Origin of Life—Five Questions Worth Asking. Mungapeze timabuku timeneti kwa Mboni za Yehova za kwanuko kapena kwa ofalitsa a magazini ino.