Mawu a M'munsi
c Ngati mukufuna kuphunzira zinthu zambiri zokhudza Baibulo, kambiranani ndi Mboni za Yehova za m’dera lanu. Kapena lembani kalata pogwiritsa ntchito adiresi yoyenera pa maadiresi amene ali patsamba 5. Kapenanso mungapite pa malo athu a pa Intaneti pogwiritsa ntchito adiresi iyi: www.pr418.com.