Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti poyambirira ku America kunapita akapolo ochepa, m’kupita kwa nthawi chiwerengero cha akapolo chinawonjezereka kwambiri, makamaka chifukwa chakuti akapolowo ankakwatira n’kumabereka ana.