Mawu a M'munsi
c Kaini sanafune kumvera malangizo a Yehova. Zimene zinamuchitikira zikutiphunzitsa kuti si bwino kuchitira nsanje munthu wina ngati wachita bwino pa zinthu zinazake.—Afilipi 2:3.