Mawu a M'munsi
b Padziko lonse lapansi madokotala ambiri akuona kuti chithandizo chosagwiritsa ntchito magazi ndi chabwino kwambiri. Anthu amene amaikidwa magazi amatha kutenga kachilombo ka HIV komanso kudwala matenda ena. Anthu enanso amati akalandira magazi, thupi lawo siligwirizana nawo.