Mawu a M'munsi
a Air bag ndi kathumba kamene kamakhala pafupi ndi chiwongolero ndipo kanapangidwa kuti galimoto ikamenyetseka mwamphamvu kutsogolo, kathumbako kazikhuta mpweya n’kufwamphuka. Izi zimateteza woyendetsayo kuti asamenye chiwongolero.