Mawu a M'munsi
a Baibulo likamagwiritsa ntchito mawu akuti “mpaka kalekale,” silitanthauza kwamuyaya, kapena kuti nthawi yosatha. Mawuwa amangotanthauza nthawi yaitali kwambiri, kapena nthawi imene sikudziwika bwinobwino kuti idzathera pati.