Mawu a M'munsi
c Koma dziwani kuti nthawi zina si bwino kusunga chinsinsi. Mwachitsanzo, ngati mnzanu wachita tchimo, ali ndi maganizo ofuna kudzipha kapena ngati wayamba khalidwe linalake lotayirira, muyenera kuuza anthu ena. Kuti mudziwe zambiri zokhudza nkhani imeneyi, onani Galamukani! ya December 2008, tsamba 19 mpaka 21, ndi Galamukani! ya May 2008, tsamba 26 mpaka 29.