Mawu a M'munsi
a Buku lina linanena kuti zaka zaunyamata, ndi nthawi imene munthu amakonzekera kutsanzikana ndi makolo ake n’kukakhala payekha. Kuti mumve zambiri, onani Nsanja ya Olonda ya May 1, 2009, tsamba 10 mpaka 12, yofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.