Mawu a M'munsi
c Achinyamata amene makolo awo anali atumiki a Mulungu, Chikhristu chitayamba komanso chisanayambe, ankachita zinthu ndi anthu akuluakulu. Zikuoneka kuti pa nthawi imeneyo panalibe kusiyana pakati pa wachinyamata ndi munthu wachikulire.