Mawu a M'munsi
b Anthu amene amati zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina, amakhulupirira kuti zimenezi zinachitika pa zifukwa zosiyanasiyana, monga kusintha kwa nyengo ndi zina zotero. M’nkhani yotsatira tikambirana mwachidule zimenezi.