Mawu a M'munsi
a Wasayansi wina, dzina lake Ernst Mayr, ngakhale kuti amakhulupirira kuti zamoyo zinachita kusintha, ananena kuti: “Mafupa a nyama ofukulidwa pansi sasonyeza kuti zamoyo zinkasintha pang’onopang’ono n’kukhala za mtundu wina.”