Mawu a M'munsi
b N’zoona kuti mphamvu yochokera ku dzuwa komanso makemikolo imatha kusintha DNA. Koma kusintha kumeneku sikumachititsa kuti zamoyo zisinthe n’kukhala zamtundu wina. Onani nkhani yakuti “Kodi Chisinthiko Chinachitikadi?” mu Galamukani! ya September 2006.