Mawu a M'munsi
a Ku Mexico kuli mitundu 136 ya zomera zimenezi. Mitundu ingapo amaigwiritsa ntchito pofulula mowa wa pulque ndi zakumwa zina zaukali. Koma mtundu wa bluu wokha wa zomerazi ndi umene amapangira mowa wa tequila.